Edge Rewrite
// HTMLRewriter · presentation

This page was redesigned at the edge.

Cloudflare fetched the original article and streamed it through HTMLRewriter to apply an entirely new visual system without rebuilding the source page.

Jump to content

Talk:Samuel Kawale

Page contents not supported in other languages.
Add topic
From Wikipedia, the free encyclopedia
Latest comment: 1 year ago by 137.196.0.28 in topic Honorable

Honorable

[edit]

Zipangizo za ulimi zotsika mtengo. Boma linatiganizila ife a Malawi osaukitsitsa kuti tithe kufikila kugula zipangozozi kuno kwathu kwa Chimpumbulu T/A Chitukula, Lilongwe koma zomwe zikuchitika ndi dzinyengo anthu omwe mwawatuma kuti adzatigulitse zipangizozi kuti munthu agule ayeneleka kupelekanso ndalama ya lunch kuwonjezela apo omwe akugula zipangizozi ndi mavenda okha okha ife anthu akumudzi tikupempha kuti mutibweletsele achitetezo.Mwina anthu omwe mwawatuma wa ndi a opposition iyi a kupangayi ndi dikampeni yoti a Malawi ade kukhosi ndi Boma lomwe likulamulilali.Chonde bwana tithandizeni 137.196.0.28 (talk) 03:18, 13 November 2024 (UTC)Reply